Kodi Ababa Surgent wayamba Kuyimba nyimbo za Amapiano???
by Charles Magwira

Atati Ziii Kwa Nthawi yaitali, New Baby Father yemwe amaziwikaso kuti Star Bouy Ababa Surgent, Wavumbuluka ndi Nyimbo Ya Tsopano yotchedwa "Tili Pompo" imene yajambulidwa ndi Stich Fray wa D&T Records.

Koma Chasisa Zaye kuti Njobvu itchyoke Nyanga ndi Choti, oyimbayu wayimba Amapiano, pomwe anthu amaziwa bwino lomwe kuti iyeyo amayimba Dancehall.

Poyankhulana ndi Ghetto Tunes, Ababa Surgent wanenesa kuti mau ake ndi omwe aja ah Dancehall zangosintha ndi zin"gwenyen"gwenye kapena kuti instruments.

Despite the silence, Ababa wa Kapruuuum nation wakhala akupanga record nyimbo as he is fully passionate ndi Nyimbo za Dancehall.

Mu mbiri ya Nyimbo ino Ababa Surgent sakhala oyamba kusintha kaimbidwe ka Nyimbo zake, oyimba ena omwe ankaziwika bwino ndi Nyimbo za Reggae/dancehall ngati Stich Fray, Saint ndi ena ambili anasinthaso maimbidwe a nyimbo zao.

Mverani kapena Tsisani Ababa Surgent Tili Pompo munsimu http://ghettotunes.com/stream?a=76102

.

.

.

.